Marko 1:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yohane anabvala ubweya wa ngamila, ndi lamba lacikopa m'cuuno mwace, nadya dzombe ndi uci wa kuthengo.

Marko 1

Marko 1:1-7