Marko 1:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaturuka a ku dziko lonse la Yudeya, ndi a ku Yerusalemu onse; nadza kwa iye nabatizidwa ndi iye mumtsinje Yordano, poulula macimo ao.

Marko 1

Marko 1:1-9