Maliro 3:65-66 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Muphimbe mtima wao ndi kuwatemberera; Mudzawalondola mokwiya ndi kuwaononga pansi pa thambo la Yehova.