Maliro 2:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwaitana zondiopsya mozungulira ngati tsiku la msonkhano;Panalibe wopulumuka ndi wotsala tsiku la mkwiyo wa Yehova;Omwe ndinawaseweza ndi kuwalera, adaniwo anawatsiriza.

Maliro 2

Maliro 2:19-22