Maliro 3:64-66 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Mudzawabwezera cilango, Yehova, monga mwa macitidwe a manja ao; Muphimbe mtima wao ndi kuwatemberera;