Maliro 3:47-50 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

47. Mantha ndi dzenje zitifikira, ndiphokose ndi cionongeko.

48. M'diso mwanga mutsikamitsinje ya madzi cifukwa ca mwana wamkazi wa anthu amtundu wanga woonongedwa,

49. Diso langa lingotsanulira osaleka, osapumula,

50. Kufikira Yehova adzazolika kumwamba ndi kuona;

Maliro 3