Maliro 3:43-46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

43. Mwadzikuta ndi mkwiyo ndi kutilondola, mwatipha osacitira cisoni.

44. Mwadzikuta ndi mtambo kuti pemphero lathu lisapyolemo.

45. Mwatiika pakati pa amitundu ngati zinyalala ndi za kudzala.

46. Adani athu onse anatiyasamira,

Maliro 3