Maliro 2:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zipata zace zalowa pansi; waononga ndi kutyola mipiringidzo yace;Mfumu yace ndi akalonga ace ali pakati pa amitundu akusowa cilamulo;Inde, aneneri ace samalandira masomphenya kwa Yehova.

Maliro 2

Maliro 2:5-19