Maliro 2:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova watsimikiza mtima kupasula linga la mwana wamkazi wa Ziyoni;Watambalika cingwe, osabweza dzanja lace kuti lisaonongepo;Waliritsa chemba ndi linga; zilefuka pamodzi.

Maliro 2

Maliro 2:3-12