Maliro 2:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Aneneri ako anakuonera masomphenya acabe ndi opusa;Osaulula mphulupulu yako kuti abweze undende wako,Koma anakuonera manenero acabe ndi opambutsa.

Maliro 2

Maliro 2:9-21