Maliro 2:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ambuye waphimbatu ndi mtambo mwana wamkazi wa Ziyoni, pomkwiyira!Wagwetsa pansi kucokera kumwamba kukoma kwace kwa Israyeli;Osakumbukira poponda mapazi ace tsiku la mkwiyo wace.

Maliro 2

Maliro 2:1-5