Macitidwe 3:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mulungu wa Abrahamu, ndi Isake, ndi Yakobo, Mulungu wa makolo athu, analemekeza Mwana wace Yesu; amene, inu munampereka ndi kumkaniza pa Pilato, poweruza iyeyu kummasula.

Macitidwe 3

Macitidwe 3:12-14