Macitidwe 3:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma m'mene Petro anaciona, anayankha kwa anthu, Amuna inu a Israyeli, muzizwa naye bwanji ameneyo? kapena mutipenyetsetsa ife bwanji, monga ngati tamyendetsa iye ndi mphamvu ya ife eni, kapena ndi cipembedzo cathu?

Macitidwe 3

Macitidwe 3:10-18