Macitidwe 28:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pamene akunjawo anaona ciromboco ciri lende pa dzanja lace, ananena wina ndi mnzace, Zoona munthuyu ndiye wambanda, angakhale anapulumuka m'nyanja, cilungamo sicimlola akhale ndi moyo.

Macitidwe 28

Macitidwe 28:1-13