Macitidwe 2:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero, pokhala mneneri iye, ndi kudziwa kuti ndi Iumbiro anamlumbirira Mulungu, kuti mwa cipatso ca m'cuuno mwace adzakhazika wina pa mpando wacifumu wace;

Macitidwe 2

Macitidwe 2:25-38