Macitidwe 2:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amuna inu, abale, kuloleka kunena poyera posaopa kwa inu za kholo lija Davine, kuti adamwalira naikidwanso, ndipo manda ace ali ndi ife kufikira lero lino.

Macitidwe 2

Macitidwe 2:19-30