Macitidwe 10:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pompenyetsetsa iye ndi kuopa, anati, Nciani, Mbuye? Ndipo anati kwa iye, Mapemphero ako ndi zacifundo zako zinakwera zikhala cikumbutso pamaso pa Mulungu.

Macitidwe 10

Macitidwe 10:1-13