Macitidwe 10:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye anapenya m'masomphenya poyera, mngelo wa Mulungu alinkudza kwa iye, ngati ora lacisanu ndi cinai la usana, nanena naye, Komeliyo.

Macitidwe 10

Macitidwe 10:1-9