Luka 9:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali, m'mawa mwace, atatsika m'phiri, khamu lalikuru la anthu linakomana naye.

Luka 9

Luka 9:28-41