Luka 9:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakutero mauwo, Yesu anapezedwa ali yekha. Ndipo iwo anakhala cete, ndipo sanauza munthu ali yense masiku aja kanthu konse ka izo anaziona.

Luka 9

Luka 9:31-40