Luka 9:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti anali amuna ngati zikwi zisanu. Koma iye anati kwa ophunzira ace, Khalitsani iwo pansi magulu magulu, ngati makumi asanu asanu.

Luka 9

Luka 9:6-22