Luka 7:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamene Yesu adamariza mau ace onse m'makutu a anthu, analowa m'Kapernao.

2. Ndipo kapolo wa kenturiyo, wokondedwa naye, anadwala, nafuna kutsirizika.

Luka 7