Luka 8:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, katapita kamphindi anayendayenda kumizinda ndi kumidzi, kulalikira ndi kuwauza U thenga Wabwino wa Ufumu wa Mulungu, ndi pamodzi naye khumi ndi awiriwo,

Luka 8

Luka 8:1-4