Luka 21:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzagwa ndi lupanga lakuthwa, nadzagwidwa ndende kunka ku mitundu yonse ya anthu; ndipo mapazi a anthu akunja adzapondereza kufikira kuti nthawi zao za anthu akunja zakwanira.

Luka 21

Luka 21:16-25