Luka 21:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma tsoka iwo akukhala ndi pakati, ndi iwo akuyamwitsa ana masiku awo! pakuti padzakhala cisauko cacikuru padziko, ndi mkwiyo pa anthu awa.

Luka 21

Luka 21:20-29