Luka 20:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamyang'anira, natumiza ozonda, amene anadzionetsera ngati olungama mtima, kuti akamkole pa mau ace, kotero kuti akampereke iye ku ukulu ndi ulamuliro wa kazembe.

Luka 20

Luka 20:13-21