Luka 15:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma amisonkho onse ndi anthu ocimwa analikumyandikira kudzamva iye.

2. Ndipo Afarisi ndi alembi anadandaula nati, Uyu alandira anthu ocimwa, nadya nao.

3. Koma anati kwa iwo fanizo ili, nanena,

Luka 15