Luka 16:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye ananenanso kwa ophunzira ace, Panali munthu mwini cuma, anali ndi kapitao wace; ndipo ameneyu ananenezedwa kwa iye kuti alikumwaza cuma cace.

Luka 16

Luka 16:1-2