Luka 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuyambira paciyambi, ndinayesa nkokoma inenso, amene ndinalondalonda mosamalitsa zinthu zonse kuyambira paciyambi, kulembera kwa iwe tsatane tsatane, Teofilo wabwinotu iwe;

Luka 1

Luka 1:1-4