Levitiko 9:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nunene kwa ana a Israyeli, ndi kuti, Dzitengereni tonde akhale nsembe yaucimo; ndi mwana wa ng'ombe, ndi mwana wa nkhosa, a caka cimodzi, opanda cirema, akhale nsembe yopsereza;

Levitiko 9

Levitiko 9:1-9