Levitiko 26:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Musamadzipangira mafano, kapena kudziutsira mafano osema, kapena coimiritsa, kapena kuika mwala wozokota m'dziko mwanu kuugwadira umene; popeza Ine ndine Yehova Mulungu wanu.

2. Musunge masabata anga, ndi kucitira ulemu malo anga opatulika; Ine ndine Yehova.

Levitiko 26