Levitiko 26:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musamadzipangira mafano, kapena kudziutsira mafano osema, kapena coimiritsa, kapena kuika mwala wozokota m'dziko mwanu kuugwadira umene; popeza Ine ndine Yehova Mulungu wanu.

Levitiko 26

Levitiko 26:1-2