Levitiko 25:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'phiri la Sinai, ndi kuti,

2. Nena ndi ana a Israyeli, nuti nao, Mutakalowa m'dziko limene ndikupatsani, dzikoli lizisungira Yehova Sabata.

Levitiko 25