Levitiko 24:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Aroni aikonze kunja kwa nsaru yocinga ya mboni, m'cihema cokomanako, kuyambira madzulo kufikira m'mawa, pamaso pa Yehova nthawi zonse; likhale lemba losatha mwa mibadwo yanu.

Levitiko 24

Levitiko 24:1-11