Levitiko 24:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Uza ana a Israyeli, kuti akutengere mafuta a azitona oyera opera akuunikira, kuti aziwalitsa nyali nthawi zonse.

Levitiko 24

Levitiko 24:1-8