Levitiko 23:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mulalikire tsiku lomwelo; kuti mukhale nao msonkhano wopatulika; musamagwira nchito ya masiku ena; ndilo lemba losatha m'nyumba zanu zonse, mwa mibadwo yanu yonse.

Levitiko 23

Levitiko 23:11-22