Levitiko 20:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthu wakutembenukira kwa obwebweta ndi anyanga kuwatsata ndi cigololo, nkhope yanga idzatsutsana naye munthuyo, ndipo ndidzamsadza kumcotsa pakati pa anthu a mtundu wace.

Levitiko 20

Levitiko 20:1-15