Levitiko 17:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti moyo wa nyama ukhala m'mwazi; ndipo ndakupatsani uwu pa guwa la nsembe, ucite cotetezera moyo wanu; pakuti wocita cotetezera ndiwo mwazi, cifukwa ca moyo wace.

Levitiko 17

Levitiko 17:5-12