Levitiko 17:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthu ali yense wa mbumba ya Israyeli, kapena mlendo wogonera pakati panu, wakudya mwazi uli wonse; nkhope yanga idzatsutsana naye munthu wakudya mwaziyo, ndi kumsadza kumcotsa kwa anthu a mtundu wace.

Levitiko 17

Levitiko 17:3-12