Hoseya 2:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndingambvule wamarisece, ndi kumuika ngati tsiku lija anabadwalo, ndi kumsanduliza ngati cipululu, ndi kumuika ngati dziko louma, ndi kumupha nalo ludzu;

Hoseya 2

Hoseya 2:1-4