Hoseya 2:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mutsutsane naye mai wanu, mutsutsane naye; pakuti sali mkazi wanga, ndi Ine sindiri mwamuna wace; ndipo acotse zadama zace pankhope pace, ndi zigololo zace pakati pa maere ace;

Hoseya 2

Hoseya 2:1-10