Hoseya 14:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo okhala pansi pa mthunzi wace adzabwera, nadzatsitsimuka ngati tirigu, nadzaphuka ngati mpesa, cikumbukilo cace cidzanga vinyo wa Lebano.

Hoseya 14

Hoseya 14:1-9