Hoseya 13:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Ine ndine Yehova Mulungu wako cicokere m'dziko la Aigupto, ndipo suyenera kudziwa mulungu wina koma Ine; ndi popanda Ine palibe mpulumutsi.

Hoseya 13

Hoseya 13:1-5