Hoseya 13:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace adzakhala ngati mtambo wa m'mawa, ndi ngati mame asansuka mamawa, ngati mungu umene mphepo iuuluza kudwale, ndi ngati utsi woturuka kukafwambira.

Hoseya 13

Hoseya 13:1-13