Genesis 7:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati Yehova kwa Nowa, Talowani, iwe ndi a ku nyumba ako onse m'cingalawamo; cifukwa ndakuona iwe kuti uli wolungama pamaso panga m'mbadwo uno.

Genesis 7

Genesis 7:1-6