Genesis 6:21-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

21. Ndipo iwe udzitengereko wekha zakudya zonse zodyedwa, oudzisonkhanitsire izi wekha: ndipo zidzakhala zakudya za iwe ndi za iwo.

22. Cotero anacita Nowa, monga mwa zonse anamlamulira iye Mulungu, momwemo anacita.

Genesis 6