Genesis 49:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Adamanga mwana wa kavalo wace pampesa,Ndi mwana wa buru wace pa mpesa wosankhika;Natsuka malaya ace m'vinyo,Ndi copfunda cace m'mwazi wa mphesa.

Genesis 49

Genesis 49:4-20