Genesis 49:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndodo yacifumu siidzacoka mwa Yuda,Kapena wolamulira pakati pa mapazi ace,Kufikira atadza Silo;Ndipo anthu adzamvera iye.

Genesis 49

Genesis 49:2-14