Genesis 45:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamfotokozera iye mau onse a Yosefe amene ananena ndi iwo; ndipo pamene anaona magareta amene Yosefe anatumiza kuti amtengeremo, mtima wa Yakobo atate wao unatsitsimuka;

Genesis 45

Genesis 45:24-28