Genesis 44:13-15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

13. ndipo anang'amba zobvala zao, nasenzetsa yense buru wace, nabwera kumuzi.

14. Yudanso ndi abale ace anadza cu nyumba ya Yosefe; ndipo iye ikali pamenepo; ndipo anagwa oansi patsogolo pace.

15. Ndipo losefe anati kwa iwo, Ici nciani nwacicita? Kodi simudziwa kuti nunthu ngati ine ndingathe kuzindidra ndithu?

Genesis 44